Luka 3:4 - Buku Lopatulika4 monga mwalembedwa m'buku la Yesaya mneneri, kuti, Mau a wofuula m'chipululu, konzani khwalala la Ambuye, lungamitsani njira zake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 monga mwalembedwa m'buku la Yesaya mneneri, kuti, Mau a wofuula m'chipululu, konzani khwalala la Ambuye, lungamitsani njira zake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Izi zidachitika monga zidaalembedwera m'buku la mneneri Yesaya kuti, “Liwu la munthu wofuula m'chipululu: akunena kuti, ‘Konzani mseu wodzadzeramo Ambuye, ongolani njira zoti adzapitemo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Monga analembera mʼbuku la Yesaya mneneri kuti: “Mawu a wofuwula mʼchipululu, konzani njira ya Ambuye, wongolani njira zake. Onani mutuwo |