Luka 3:15 - Buku Lopatulika15 Ndipo pamene anthu anali kuyembekezera, ndipo onse anaganizaganiza m'mitima yao za Yohane, ngati kapena iye ali Khristu; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Ndipo pamene anthu anali kuyembekezera, ndipo onse anaganizaganiza m'mitima yao za Yohane, ngati kapena iye ali Khristu; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Chiyembekezo cha anthu chidayamba kukula, ndipo onse ankaganiza za Yohane kuti kapena ndiye Mpulumutsi wolonjezedwa uja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Anthu ankadikira ndi chiyembekezo ndipo ankasinkhasinkha mʼmitima mwawo kuti mwina Yohane nʼkukhala Khristu. Onani mutuwo |