Luka 3:13 - Buku Lopatulika13 Koma iye anati kwa iwo, Musakapambe kanthu konse kakuposa chimene anakulamulirani. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Koma iye anati kwa iwo, Musakapambe kanthu konse kakuposa chimene anakulamulirani. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Iye adati, “Musamakhometsa msonkho moonjezera pa zimene adakulamulani.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Iye anawawuza kuti, “Musalandire moposa zimene muyenera.” Onani mutuwo |