Luka 3:12 - Buku Lopatulika12 Ndipo amisonkho omwe anadza kudzabatizidwa, nati kwa iye, Mphunzitsi, ife tizichita chiyani? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndipo amisonkho omwe anadza kudzabatizidwa, nati kwa iye, Mphunzitsi, ife tizichita chiyani? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Kudabweranso okhometsa msonkho kuti Yohane aŵabatize. Iwo adamufunsa kuti, “Aphunzitsi, kodi ife tizichita zabwino zanji?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Amisonkho nawonso anabwera kudzabatizidwa. Iwo anafunsa kuti, “Aphunzitsi, ife tichite chiyani?” Onani mutuwo |