Luka 24:53 - Buku Lopatulika53 ndipo anakhala chikhalire mu Kachisi, nalikuyamika Mulungu. Amen. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201453 ndipo anakhala chikhalire m'Kachisi, nalikuyamika Mulungu. Amen. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa53 Tsono ankasonkhana m'Nyumba ya Mulungu nthaŵi ndi nthaŵi akutamanda Mulungu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero53 Ndipo iwo anakhalabe ku Nyumba ya Mulungu, akulemekeza Mulungu. Onani mutuwo |