Luka 24:43 - Buku Lopatulika43 Ndipo anachitenga, nachidya pamaso pao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201443 Ndipo anachitenga, nachidya pamaso pao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa43 Iye atalandira nsombayo, adaidya iwo akuwona. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero43 Iye anakatenga ndi kukadya iwo akuona. Onani mutuwo |