Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Luka 24:42 - Buku Lopatulika

42 Ndipo anampatsa Iye chidutsu cha nsomba yokazinga.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

42 Ndipo anampatsa Iye chidutsu cha nsomba yokazinga.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

42 Adampatsa chidutsu cha nsomba yootcha.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

42 Iwo anamupatsa Iye kachidutswa ka nsomba yophika.

Onani mutuwo Koperani




Luka 24:42
4 Mawu Ofanana  

Ndipo anawalamulira kwambiri kuti asadziwe ichi munthu mmodzi, nawauza kuti ampatse iye kudya.


Koma pokhala iwo chikhalire osakhulupirira chifukwa cha chimwemwe, nalikuzizwa, anati kwa iwo, Muli nako kanthu kakudya kuno?


Ndipo anachitenga, nachidya pamaso pao.


Yesu anadza natenga mkate napatsa iwo, momwemonso nsomba.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa