Luka 24:20 - Buku Lopatulika20 ndi kuti ansembe aakulu ndi akulu athu anampereka Iye ku chiweruziro cha imfa, nampachika Iye pamtanda. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 ndi kuti ansembe aakulu ndi akulu athu anampereka Iye ku chiweruziro cha imfa, nampachika Iye pamtanda. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Akulu a ansembe ndi akulu athu ena adampereka kuti azengedwe mlandu ndi kuphedwa, ndipo adampachika pa mtanda. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Akulu a ansembe ndi oweruza anamupereka Iye kuti aphedwe, ndipo anamupachika Iye; Onani mutuwo |