Luka 24:11 - Buku Lopatulika11 Ndipo mau awa anaoneka pamaso pao ngati nkhani zachabe, ndipo sanamvere akaziwo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Ndipo mau awa anaoneka pamaso pao ngati nkhani zachabe, ndipo sanamvere akaziwo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Koma zimenezo atumwiwo adangoziyesa zam'kutu, mwakuti sadaŵakhulupirire azimaiwo. [ Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Koma iwo sanawakhulupirire amayiwa, chifukwa mawu awo amaoneka kwa iwo ngati opanda nzeru. Onani mutuwo |