Luka 24:12 - Buku Lopatulika12 Koma Petro ananyamuka nathamangira kumanda, ndipo powerama anaona nsalu zabafuta pazokha; ndipo anachoka nanka kwao, nazizwa ndi chija chidachitikacho. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Koma Petro ananyamuka nathamangira kumanda, ndipo powerama anaona nsalu zoyera pa zokha; ndipo anachoka nanka kwao, nazizwa ndi chija chidachitikacho. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Komabe Petro adanyamuka nathamangira ku manda. Adaŵeramiramo naona nsalu zamaliro zokha, kenaka nkubwerera kunyumba akudabwa ndi zimene zidaachitikazo.] Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Komabe Petro anayimirira ndi kuthamangira ku manda. Atasuzumira, anaona nsalu zimene anamukulungira zija zili pa zokha, ndipo iye anachoka, akudabwa ndi zimene zinachitikazo. Onani mutuwo |