Luka 23:4 - Buku Lopatulika4 Ndipo Pilato anati kwa ansembe aakulu ndi makamu a anthu, Ndilibe kupeza chifukwa cha mlandu ndi munthu uyu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ndipo Pilato anati kwa ansembe aakulu ndi makamu a anthu, Ndilibe kupeza chifukwa cha mlandu ndi munthu uyu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Pamenepo Pilato adauza akulu a ansembe ndi anthu onse aja kuti, “Sindikumpeza mlandu munthuyu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Kenaka Pilato anawawuza akulu a ansembe ndi gulu la anthu, “Ine sindikumupeza cholakwa munthuyu.” Onani mutuwo |