Luka 22:34 - Buku Lopatulika34 Ndipo Iye anati, Ndikuuza iwe, Petro, sadzalira tambala lero lino kufikira udzakana katatu kuti sundidziwa Ine. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201434 Ndipo Iye anati, Ndikuuza iwe, Petro, sadzalira tambala lero lino kufikira udzakana katatu kuti sundidziwa Ine. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa34 Koma Yesu adamuyankha kuti, “Ndikukuuza, iwe Petro, kuti lero lomwe lino, tambala asanalire, ukhala utandikana katatu kuti Ine sundidziŵa.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero34 Yesu anayankha kuti, “Ine ndikukuwuza Petro, tambala asanalire lero lino, udzandikana katatu kuti sukundidziwa Ine.” Onani mutuwo |