Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Luka 22:33 - Buku Lopatulika

33 Ndipo anati kwa Iye, Ambuye, ndilipo ndikapite ndi Inu kundende ndi kuimfa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

33 Ndipo anati kwa Iye, Ambuye, ndilipo ndikapite ndi Inu kundende ndi kuimfa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

33 Apo Petro adati, “Ambuye, ndili wokonzeka kupita nanu ku ndende, ngakhale kufa kumene.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

33 Koma iye anayankha kuti, “Ambuye, ndine wokonzeka kupita nanu ku ndende ndi kufa komwe.”

Onani mutuwo Koperani




Luka 22:33
16 Mawu Ofanana  

Wokhulupirira mtima wakewake ali wopusa; koma woyenda mwanzeru adzapulumuka.


Inu Yehova, ndidziwa kuti njira ya munthu sili mwa iye mwini; sikuli kwa munthu woyenda kulongosola mapazi ake.


Mtima ndiwo wonyenga koposa, ndi wosachiritsika, ndani angathe kuudziwa?


Koma Yesu anayankha nati, Inu simudziwa chimene mupempha. Kodi mukhoza kumwera chikho nditi ndidzamwere Ine? Iwo ananena kwa Iye, Ife tikhoza.


Koma Petro ananena naye, Angakhale adzakhumudwa onse, komatu ine iai.


Koma iye analimbitsa mau chilimbitsire, kuti, Ngakhale ndidzafa nanu, sindidzakana Inu. Ndipo onsewo anatero.


Ndipo Iye anati, Ndikuuza iwe, Petro, sadzalira tambala lero lino kufikira udzakana katatu kuti sundidziwa Ine.


Koma anakana, nati, Mkaziwe, sindimdziwa Iye.


Yesu anayankha, Moyo wako kodi udzautaya chifukwa cha Ine? Indetu, indetu, ndinena kwa iwe, Asanalire tambala udzandikana Ine katatu.


Pamenepo Paulo anayankha, Muchitanji, polira ndi kundiswera mtima? Pakuti ndakonzeka ine si kumangidwa kokha, komatunso kufera ku Yerusalemu chifukwa cha dzina la Ambuye Yesu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa