Luka 21:7 - Buku Lopatulika7 Ndipo iwo anamfunsa Iye, nati, Mphunzitsi, nanga zinthu izi zidzaoneka liti? Ndipo chizindikiro ndi chiyani pamene izi ziti zichitike? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ndipo iwo anamfunsa Iye, nati, Mphunzitsi, nanga zinthu izi zidzaoneka liti? Ndipo chizindikiro ndi chiyani pamene izi ziti zichitike? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Anthu aja adafunsa Yesu kuti, “Aphunzitsi, zimenezi zidzachitika liti? Tidzaonera chiyani kuti zonsezi zili pafupi kuchitika?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Iwo anafunsa kuti, “Aphunzitsi, kodi zonsezi zidzachitika liti? Ndipo tidzaonera chiyani kuti zili pafupi kuchitika?” Onani mutuwo |