Luka 21:32 - Buku Lopatulika32 Indetu ndinena ndinu, Mbadwo uno sudzapitirira, kufikira zonse zitachitika. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201432 Indetu ndinena ndinu, Mbadwo uno sudzapitirira, kufikira zonse zitachitika. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa32 Ndithu ndikunenetsa kuti zonsezi zidzaoneka anthu a mbadwo unoŵa asanamwalire onse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero32 “Zoonadi, Ine ndikukuwuzani kuti mʼbado uno sudzatha mpaka zinthu zonsezi zitachitika. Onani mutuwo |