Luka 21:31 - Buku Lopatulika31 Inde chotero inunso, pakuona zinthu izi zilikuchitika, zindikirani kuti Ufumu wa Mulungu uli pafupi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201431 Inde chotero inunso, pakuona zinthu izi zilikuchitika, zindikirani kuti Ufumu wa Mulungu uli pafupi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa31 Momwemonso, mukadzaona zija ndanenazi zikuchitika, mudzadziŵe kuti ufumu wa Mulungu uli pafupi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero31 Chimodzimodzinso, mukadzaona zinthu zonsezi, dziwani kuti ufumu wa Mulungu uli pafupi. Onani mutuwo |