Luka 21:30 - Buku Lopatulika30 pamene iphukira, muipenya nimuzindikira pa nokha kuti dzinja lili pafupi pomwepo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201430 pamene iphukira, muipenya nimuzindikira pa nokha kuti dzinja lili pafupi pomwepo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa30 Mukamaona kuti masamba akuphuka, mumadziŵa kuti chilimwe chayandikira kale. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero30 Ikamatulutsa masamba, mumakhoza kudzionera nokha ndi kudziwa kuti dzinja lili pafupi. Onani mutuwo |