Luka 20:14 - Buku Lopatulika14 Koma olimawo, pamene anamuona, anauzana wina ndi mnzake, nati, Uyu ndiye wolowa nyumba; tiyeni timuphe, kuti cholowa chake chikhale chathu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Koma olimawo, pamene anamuona, anauzana wina ndi mnzake, nati, Uyu ndiye wolowa nyumba; tiyeni timuphe, kuti cholowa chake chikhale chathu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Koma alimi aja atamuwona, adayamba kuuzana kuti, ‘Uyu ndiye amene adzamsiyire chumachi. Tiyeni timuphe kuti chidzakhale chathu.’ Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 “Koma alimiwo ataona mwanayo, anakambirananso. Iwo anati, ‘Uyu ndiye wodzamusiyira chumachi. Tiyeni timuphe ndipo chumachi chikhala chathu.’ Onani mutuwo |