Luka 20:15 - Buku Lopatulika15 Ndipo anamponya kunja kwa mundawo, namupha. Pamenepo mwini munda wampesawo adzawachitira chiyani? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Ndipo anamponya kunja kwa mundawo, namupha. Pamenepo mwini munda wamphesawo adzawachitira chiyani? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Tsono adamuponya kunja kwa mundawo, namupha. Kodi mwini munda wamphesa uja adzaŵatani alimi aja? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Ndipo anamuponya kunja kwa mundawo ndi kumupha. “Nanga tsono mwini munda wamphesayo adzawatani anthuwa? Onani mutuwo |