Luka 2:9 - Buku Lopatulika9 Ndipo mngelo wa Ambuye anaimirira pa awo, ndi kuwala kwa Ambuye kunawaunikira kozungulira: ndipo anaopa ndi mantha aakulu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndipo mngelo wa Ambuye anaimirira pa awo, ndi kuwala kwa Ambuye kunawaunikira kozungulira: ndipo anaopa ndi mantha akulu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Mwadzidzidzi mngelo wa Ambuye adadzaimirira pakati pao, ndipo ulemerero wa Ambuye udaŵala ponse pozungulira, mwakuti abusawo adaachita mantha kwambiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Mngelo wa Ambuye anaonekera kwa iwo ndipo ulemerero wa Ambuye unawala mowazungulira. Iwo anachita mantha. Onani mutuwo |