Luka 2:52 - Buku Lopatulika52 Ndipo Yesu anakulabe m'nzeru ndi mumsinkhu, ndi m'chisomo cha pa Mulungu ndi cha pa anthu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201452 Ndipo Yesu anakulabe m'nzeru ndi mumsinkhu, ndi m'chisomo cha pa Mulungu ndi cha pa anthu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa52 Ndipo Yesu analikunka nakula m'nzeru ndi mu msinkhu, ndipo Mulungu ndi anthu omwe ankakondwera naye kwambiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero52 Ndipo Yesu anakula mu nzeru, msinkhu ndi chisomo cha Mulungu ndi anthu. Onani mutuwo |