Luka 2:47 - Buku Lopatulika47 Ndipo onse amene anamva Iye anadabwa ndi chidziwitso chake, ndi mayankho ake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201447 Ndipo onse amene anamva Iye anadabwa ndi chidziwitso chake, ndi mayankho ake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa47 Onse amene ankamva mau ake, ankadabwa ndi mayankho ake anzeru. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero47 Aliyense amene anamumva Iye anadabwa ndi chidziwitso chake ndi mayankho ake. Onani mutuwo |