Luka 2:45 - Buku Lopatulika45 ndipo pamene sanampeze, anabwera ku Yerusalemu, namfunafuna Iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201445 ndipo pamene sanampeze, anabwera ku Yerusalemu, namfunafuna Iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa45 Ataona kuti sakumpeza, adabwerera ku Yerusalemu akumufunafuna ndithu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero45 Atalephera kumupeza, anabwerera ku Yerusalemu kukamufuna. Onani mutuwo |