Luka 2:42 - Buku Lopatulika42 Ndipo pamene Iye anakhala ndi zaka zake khumi ndi ziwiri, anakwera iwo monga machitidwe a chikondwerero; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201442 Ndipo pamene Iye anakhala ndi zaka zake khumi ndi ziwiri, anakwera iwo monga machitidwe a chikondwerero; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa42 Pamene Yesu anali ndi zaka khumi ndi ziŵiri, iwo adapita kumeneko monga adaazoloŵera. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero42 Iye ali ndi zaka khumi ndi ziwiri, anapita ku phwando, monga mwa mwambo. Onani mutuwo |