Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Luka 2:28 - Buku Lopatulika

28 pomwepo iye anamlandira Iye m'manja mwake, nalemekeza Mulungu, nati,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

28 pomwepo iye anamlandira Iye m'manja mwake, nalemekeza Mulungu, nati,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

28 Pamenepo Simeoni adalandira mwanayo m'manja mwake, nayamba kutamanda Mulungu ndi mau akuti,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

28 Simeoni anamunyamula mʼmanja mwake nayamika Mulungu, nati:

Onani mutuwo Koperani




Luka 2:28
13 Mawu Ofanana  

Sekerani mwa Yehova, ndimo kondwerani inu olungama mtima; ndipo fuulani mokondwera nonsenu oongoka mtima.


Ndipo Iye anatiyangata, natidalitsa, ndi kuika manja ake pa ito.


Ndipo anatenga kamwana, nakaika pakati pao, nakayangata, nanena nao,


Ndipo Maria anati, Moyo wanga ulemekeza Ambuye,


Ndipo pomwepo panatseguka pakamwa pake, ndi lilime lake linamasuka, ndipo iye analankhula, nalemekeza Mulungu.


Wolemekezeka Ambuye, Mulungu wa Israele; chifukwa Iye anayang'ana, nachitira anthu ake chiombolo.


Ndipo abusawo anabwera, nalemekeza ndi kutamanda Mulungu pa zinthu zonse anazimva, naziona, monga kunalankhulidwa kwa iwo.


Ndipo iye analowa ku Kachisi ndi Mzimu: ndipo pamene atate ndi amake analowa ndi kamwanako Yesu, kudzamchitira Iye mwambo wa chilamulo,


Tsopano, Ambuye, monga mwa mau anu aja, lolani ine, kapolo wanu, ndichoke mumtendere;


Ndipo mauwo anakomera ana a Israele pamaso pao; ndi ana a Israele analemekeza Mulungu, osanenanso za kuwakwerera ndi kuwathira nkhondo, kuliononga dziko lokhalamo ana a Rubeni ndi ana a Gadi.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa