Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Luka 19:32 - Buku Lopatulika

32 Ndipo anachoka otumidwawo, napeza monga adanena kwa iwo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

32 Ndipo anachoka otumidwawo, napeza monga adanena kwa iwo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

32 Aŵiriwo adapita, nakapezadi monga momwe Yesu adaaŵauzira.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

32 Otumidwawo anapita nakamupeza mwana wabulu monga momwe Yesu anawawuzira.

Onani mutuwo Koperani




Luka 19:32
3 Mawu Ofanana  

Ndipo munthu akati kwa inu, Mummasuliranji? Mudzatero naye, Ambuye amfuna iye.


Ndipo pamene anamasula mwana wa bulu, eni ake anati kwa iwo, Mumasuliranji mwana wa bulu?


Ndipo anapita iwo, napeza monga adatero nao; ndipo anakonza Paska.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa