Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Luka 19:23 - Buku Lopatulika

23 ndipo sunapereke bwanji ndalama yanga pokongoletsa, ndipo ine pakudza ndikadaitenga ndi phindu lake?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

23 ndipo sunapereka bwanji ndalama yanga pokongoletsa, ndipo ine pakudza ndikadaitenga ndi phindu lake?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

23 Nanga bwanji osaiika ku banki ndalama yangayo, kuti ine pobwera ndiilandire pamodzi ndi chiwongoladzanja chake?’

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

23 Nanga nʼchifukwa chiyani sunasungitse ndalama yanga, kuti ine pobwera, ndidzayitenge ndi chiwongoladzanja?’

Onani mutuwo Koperani




Luka 19:23
6 Mawu Ofanana  

chifukwa chake ukadapereka ndalama zanga kwa okongola ndalama, ndipo ine pobwera ndikadatenga zanga ndi phindu lake.


Ananena kwa iye, Pakamwa pako ndikuweruza, kapolo woipa iwe. Unadziwa kuti ine ndine munthu wouma mtima, wonyamula chimene sindinachiike, ndi wotuta chimene sindinachifese;


Ndipo anati kwa iwo akuimirirapo, Mchotsereni minayo, nimuipatse kwa iye wakukhala nazo mina khumi.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa