Luka 19:24 - Buku Lopatulika24 Ndipo anati kwa iwo akuimirirapo, Mchotsereni minayo, nimuipatse kwa iye wakukhala nazo mina khumi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 Ndipo anati kwa iwo akuimirirapo, Mchotsereni minayo, nimuipatse kwa iye wakukhala nazo mina khumi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 Atatero adauza anthu amene anali pomwepo kuti, ‘Mlandeni ndalamayi muipereke kwa amene ali ndi ndalama makumi khumiyo.’ Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 “Ndipo iye anawuza amene anayimirira pafupi kuti, ‘Tengani ndalama yake ndi kumupatsa amene ali ndi ndalama khumiyo!’ ” Onani mutuwo |