Luka 19:2 - Buku Lopatulika2 Ndipo taonani, mwamuna wotchedwa dzina lake Zakeyo; ndipo iye anali mkulu wa amisonkho, nali wachuma. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndipo taonani, mwamuna wotchedwa dzina lake Zakeyo; ndipo iye anali mkulu wa amisonkho, nali wachuma. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Kudafika munthu wina, dzina lake Zakeyo. Iyeyo anali mkulu wa okhometsa msonkho, ndipo anali wolemera. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Kunali munthu kumeneko dzina lake Zakeyu; iye anali mkulu wa wolandira msonkho ndipo anali wolemera. Onani mutuwo |