Luka 19:3 - Buku Lopatulika3 Ndipo anafuna kuona Yesu ndiye uti, ndipo sanathe, chifukwa cha khamulo, pakuti anali wamfupi msinkhu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndipo anafuna kuona Yesu ndiye uti, ndipo sanathe, chifukwa cha khamulo, pakuti anali wamfupi msinkhu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Ankafunitsitsa kuwona Yesu kuti ngwotani. Koma pakuti Zakeyoyo anali wamfupi, adalephera kumuwona chifukwa cha kuchuluka kwa anthu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Iye ankafuna kuona Yesu kuti ndani, koma pokhala wamfupi sanathe chifukwa cha gulu la anthu. Onani mutuwo |