Luka 19:18 - Buku Lopatulika18 Ndipo anadza wachiwiri, nanena, Mbuye, mina yanu yapindula mina zisanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Ndipo anadza wachiwiri, nanena, Mbuye, mina yanu yapindula mina zisanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Wachiŵiri adadza nati, ‘Ambuye, ndalama yanu ija idapindula ndalama makumi asanu.’ Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 “Wachiwiri anabwera ndipo anati, ‘Bwana, ndalama zanu zapindula zisanu zina.’ Onani mutuwo |