Luka 18:41 - Buku Lopatulika41 Ufuna ndikuchitire chiyani? Ndipo anati, Ambuye, kuti ndipenyenso. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201441 Ufuna ndikuchitire chiyani? Ndipo anati, Ambuye, kuti ndipenyenso. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa41 “Kodi ukufuna kuti ndikuchitire chiyani?” Iye adati, “Ambuye, ndikufuna kuti ndizipenyanso.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero41 “Kodi ukufuna kuti ndikuchitire chiyani?” Iye anayankha kuti, “Ambuye, ine ndifuna ndionenso.” Onani mutuwo |