Luka 18:40 - Buku Lopatulika40 Ndipo Yesu anaima, nalamulira kuti abwere naye kwa Iye; ndipo m'mene adafika pafupi, anamfunsa iye, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201440 Ndipo Yesu anaima, nalamulira kuti abwere naye kwa Iye; ndipo m'mene adafika pafupi, anamfunsa iye, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa40 Yesu adaima nalamula kuti abwere naye kwa Iye. Atafika pafupi, Yesu adamufunsa kuti, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero40 Yesu anayima nalamula kuti abwere naye kwa Iye. Atabwera pafupi, Yesu anamufunsa kuti, Onani mutuwo |