Luka 18:34 - Buku Lopatulika34 Ndipo sanadziwitse kanthu ka izi; ndi mau awa adawabisikira, ndipo sanazindikire zonenedwazo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201434 Ndipo sanadziwitse kanthu ka izi; ndi mau awa adawabisikira, ndipo sanazindikire zonenedwazo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa34 Ophunzira aja sadamvetse konse zimenezi. Tanthauzo la mau ameneŵa linali lobisika kwa iwo, nchifukwa chake sadamvetsetse zimene Yesu ankanenazo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero34 Ophunzira sanazindikire china chilichonse cha izi. Tanthauzo lake linabisika kwa iwo, ndipo sanadziwe chimene Iye amayankhula. Onani mutuwo |