Luka 17:5 - Buku Lopatulika5 Ndipo atumwi anati kwa Ambuye, Mutionjezere chikhulupiriro. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndipo atumwi anati kwa Ambuye, Mutionjezere chikhulupiriro. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Atumwi adapempha Ambuye kuti, “Mutiwonjezere chikhulupiriro.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Atumwiwo anati kwa Ambuye, “Kulitsani chikhulupiriro chathu!” Onani mutuwo |