Luka 17:23 - Buku Lopatulika23 Ndipo adzanena ndi inu, Taonani ilo! Taonani ili? Musachoka kapena kuwatsata; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Ndipo adzanena ndi inu, Taonani ilo! Taonani ili? Musachoka kapena kuwatsata; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Anthu azidzakuuzani kuti, ‘Suuwo uli uko,’ kapena, ‘Suuwu uli pano,’ musadzapiteko kapena kuŵatsatira ai. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Anthu adzakuwuzani kuti, ‘Uyo ali apoyo!’ kapena ‘Uyu ali apa!’ Musawathamangire iwo. Onani mutuwo |