Luka 17:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo anati kwa ophunzira ake, Sikutheka kuti zolakwitsa zisadze; koma tsoka iye amene adza nazo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo anati kwa ophunzira ake, Sikutheka kuti zolakwitsa zisadze; koma tsoka iye amene adza nazo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Yesu adauza ophunzira ake kuti, “Zochimwitsa anthu sizingalephere kuwoneka, koma tsoka kwa munthu wobwera nazoyo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Yesu anati kwa ophunzira ake, “Zinthu zimene zimachimwitsa sizingalephere kubwera, koma tsoka kwa munthu wozibweretsayo. Onani mutuwo |