Luka 16:18 - Buku Lopatulika18 Yense wakusudzula mkazi wake, nakwatira wina, achita chigololo; ndipo iye amene akwatira wosudzulidwayo, achita chigololo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Yense wakusudzula mkazi wake, nakwatira wina, achita chigololo; ndipo iye amene akwatira wosudzulidwayo, achita chigololo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 “Aliyense amene asudzula mkazi wake, nakwatira wina, akuchita chigololo. Ndipo amene akwatira mkazi wosudzulidwayo, nayenso akuchita chigololo.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 “Aliyense amene asiya mkazi wake ndi kukakwatira mkazi wina akuchita chigololo, ndipo mwamuna amene akwatira mkazi wosiyidwayo akuchitanso chigololo.” Onani mutuwo |