Luka 15:32 - Buku Lopatulika32 Koma kudayenera kuti tisangalale ndi kukondwerera: chifukwa mng'ono wako uyu anali wakufa ndipo ali ndi moyo; anatayika, ndipo wapezeka. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201432 Koma kudayenera kuti tisangalale ndi kukondwerera: chifukwa mng'ono wako uyu anali wakufa ndipo ali ndi moyo; anatayika, ndipo wapezeka. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa32 Kunayenera kuti tikondwere ndi kusangalala, chifukwa mng'ono wakoyu adaafa, koma tsopano wakhalanso moyo; adaatayika, koma tsopano wapezeka.’ ” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero32 Koma tinayenera kukondwera ndi kusangalala, chifukwa mʼbale wako uyu anali wakufa ndipo ali ndi moyonso; iye anali wotayika ndipo wapezeka.” Onani mutuwo |