Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Luka 15:23 - Buku Lopatulika

23 ndipo idzani naye mwanawang'ombe wonenepa, mumuphe, ndipo tidye, tisekere;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

23 ndipo idzani naye mwanawang'ombe wonenepa, mumuphe, ndipo tidye, tisekere;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

23 Ndipo katengeni mwanawang'ombe wonenepa uja, muphe kuti tidye, tikondwere.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

23 Bweretsani mwana wangʼombe wonenepa ndipo iphani. Tiyeni tikhale ndi phwando ndi kukondwerera.

Onani mutuwo Koperani




Luka 15:23
10 Mawu Ofanana  

Ndipo Abrahamu anafulumira kunka kuzoweta, natenga kamwana ka ng'ombe kofewa ndi kabwino, napatsa mnyamata, ndipo anafulumira kuphika.


Mudzakhutitsa moyo wanga ngati ndi mafuta ndi zonona; ndipo pakamwa panga ndidzakulemekezani ndi milomo yakufuula mokondwera.


Kudya masamba, pali chikondano, kuposa ng'ombe yonenepa pali udani.


yaphera nyama yake, nisakaniza vinyo wake, nilongosolanso pa gome lake.


Ndipo m'phiri limeneli Yehova wa makamu adzakonzera anthu ake onse phwando la zinthu zonona, phwando la vinyo wa pamitsokwe, la zinthu zonona za mafuta okhaokha, la vinyo wansenga wokuntha bwino.


Koma atateyo ananena kwa akapolo ake, Tulutsani msanga mwinjiro wokometsetsa, nimumveke; ndipo mpatseni mphete kudzanja lake ndi nsapato kumapazi ake;


chifukwa mwana wanga uyu anali wakufa, ndipo akhalanso wamoyo; anali wotayika, ndipo wapezedwa. Ndipo anayamba kusekera.


Ndipo mkaziyo anali ndi mwanawang'ombe wonenepa m'nyumbamo; ndipo anafulumira, namupha, natenga ufa naukanyanga mkate wopanda chotupitsa;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa