Luka 15:2 - Buku Lopatulika2 Ndipo Afarisi ndi alembi anadandaula nati, Uyu alandira anthu ochimwa, nadya nao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndipo Afarisi ndi alembi anadandaula nati, Uyu alandira anthu ochimwa, nadya nao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Tsono Afarisi ndi aphunzitsi a Malamulo adayamba kuŵinya nkumanena kuti, “Munthu uyu amalandira anthu ochimwa, nkumadya nawo pamodzi.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Koma Afarisi ndi aphunzitsi amalamulo amangʼungʼudza nati, “Munthu uyu amalandira ochimwa ndi kudya nawo.” Onani mutuwo |