Luka 15:1 - Buku Lopatulika1 Koma amisonkho onse ndi anthu ochimwa analikumyandikira kudzamva Iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Koma amisonkho onse ndi anthu ochimwa analikumyandikira kudzamva Iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Anthu onse okhometsa msonkho ndi Ayuda enanso onyozera Malamulo ankabwera kwa Yesu kudzamva mau ake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Tsopano amisonkho ndi “ochimwa” ankasonkhana kudzamvera mawu ake. Onani mutuwo |