Luka 13:9 - Buku Lopatulika9 ndipo ngati udzabala chipatso kuyambira pamenepo, chabwino; koma ngati iai, mudzaulikhatu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 ndipo ngati udzabala chipatso kuyambira pamenepo, chabwino; koma ngati iai, mudzaulikhatu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Ukadzabala zipatso chaka chamaŵa, zidzakhala bwino. Koma ukakapanda kubala, apo mudzaudule.’ ” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Ngati udzabale zipatso chaka chamawa, zili bwino! Koma ngati sudzabala, pamenepo mudzawudule.’ ” Onani mutuwo |