Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Luka 13:10 - Buku Lopatulika

10 Ndipo analikuphunzitsa m'sunagoge mwina, tsiku la Sabata.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

10 Ndipo analikuphunzitsa m'sunagoge mwina, tsiku la Sabata.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

10 Tsiku lina la Sabata Yesu ankaphunzitsa m'nyumba ina yamapemphero.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

10 Pa Sabata Yesu ankaphunzitsa mʼsunagoge ina,

Onani mutuwo Koperani




Luka 13:10
4 Mawu Ofanana  

Ndipo Yesu anayendayenda mu Galileya monse, analikuphunzitsa m'masunagoge mwao, nalalikira Uthenga Wabwino wa Ufumu, nachiritsa nthenda zonse ndi kudwala konse mwa anthu.


ndipo ngati udzabala chipatso kuyambira pamenepo, chabwino; koma ngati iai, mudzaulikhatu.


Ndipo Iye analikulalikira m'masunagoge a ku Yudeya.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa