Luka 13:26 - Buku Lopatulika26 pomwepo mudzayamba kunena, Ife tinadya ndi kumwa pamaso panu, ndipo munaphunzitsa m'makwalala a kwathu; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 pomwepo mudzayamba kunena, Ife tinadya ndi kumwa pamaso panu, ndipo munaphunzitsa m'makwalala a kwathu; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 Apo inuyo mudzayamba kunena kuti, ‘Pajatu tinkadya ndi kumamwa nanu pamodzi, ndipo Inuyo munkaphunzitsa m'miseu ya m'mizinda mwathu.’ Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 “Ndipo inu mudzati, tinkadya ndi kumwa ndi inu ndipo munkaphunzitsa mʼmisewu yathu. Onani mutuwo |