Luka 12:6 - Buku Lopatulika6 Kodi mpheta zisanu sizigulidwa timakobiri tiwiri? Ndipo palibe imodzi ya izo iiwalika pamaso pa Mulungu; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Kodi mpheta zisanu sizigulidwa timakobiri tiwiri? Ndipo palibe imodzi ya izo iiwalika pamaso pa Mulungu; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 “Suja amagulitsa atimba asanu tindalama tiŵiri? Komabe Mulungu saiŵala ndi mmodzi yemwe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Kodi atimba asanu samagulidwa ndi ndalama ziwiri? Ngakhale zili chomwecho palibe imodzi ya izo imene imayiwalika ndi Mulungu. Onani mutuwo |