Luka 12:54 - Buku Lopatulika54 Koma Iye ananenanso kwa makamu a anthu, Pamene paliponse muona mtambo wokwera kumadzulo, pomwepo munena, kuti, Ikudza mvula; ndipo itero. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201454 Koma Iye ananenanso kwa makamu a anthu, Pamene paliponse muona mtambo wokwera kumadzulo, pomwepo munena, kuti, Ikudza mvula; ndipo itero. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa54 Yesu adauzanso anthu onse aja kuti, “Mukaona mtambo ukukwera kuzambwe, pompo mumati, ‘Mvula ikubwera,’ ndipo imabweradi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero54 Iye anati kwa gulu la anthu, “Pamene mukuona mtambo ukukwera kummawa, nthawi yomweyo inu mumati, ‘kugwa mvula,’ ndipo imagwadi. Onani mutuwo |