Luka 12:55 - Buku Lopatulika55 Ndipo pamene mphepo ya kumwera iomba, munena, kuti, Kudzakhala kutenthatu; ndipo kuterodi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201455 Ndipo pamene mphepo ya kumwera iomba, munena, kuti, Kudzakhala kutenthatu; ndipo kuterodi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa55 Mphepo yakumwera ikamaomba, mumati, ‘Kutentha,’ ndipo kumatenthadi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero55 Ndipo pamene mphepo yakummwera ikuwomba, inu mumati ‘kutentha’ ndipo kumaterodi. Onani mutuwo |