Luka 12:47 - Buku Lopatulika47 Ndipo kapolo uyo, wodziwa chifuniro cha mbuye wake, ndipo sanakonze, ndi kusachita zonga za chifuniro chakecho, adzakwapulidwa mikwapulo yambiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201447 Ndipo kapolo uyo, wodziwa chifuniro cha mbuye wake, ndipo sanakonza, ndi kusachita zonga za chifuniro chakecho, adzakwapulidwa mikwapulo yambiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa47 “Wantchito amene akudziŵa zimene mbuye wake amafuna, koma osakonzekera kuzichita, adzamkwapula kwambiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero47 “Wantchito amene amadziwa chifuniro cha mbuye wake koma wosakonzeka kapena wosachita chimene mbuye wake akufuna adzakwapulidwa zikwapu zambiri. Onani mutuwo |