Luka 12:2 - Buku Lopatulika2 Koma kulibe kanthu kovundikiridwa kamene sikadzaululidwa; ndi kobisika kamene sikadzadziwika. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Koma kulibe kanthu kovundikiridwa kamene sikadzaululidwa; ndi kobisika kamene sikadzadziwika. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Kanthu kalikonse kovundikirika kadzaululuka, ndipo kalikonse kobisika kadzadziŵika. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Palibe chinthu chophimbika chimene sichidzawululika, kapena chobisika chimene sichidzadziwika. Onani mutuwo |